![Yehovah, Mbusa wangadi, [Blues]](/_next/image?url=https%3A%2F%2Fcdn2.suno.ai%2Fimage_c157422d-34cc-4100-ae5f-b94608d24a6d.jpeg&w=384&q=75)
Yehovah, Mbusa wangadi, [Blues]
Blues electric guitar smooth yet emotive vocals expressive bends,call&response solo-driven minimalistic rhythm 12bar
August 10th, 2024suno
Lyrics
[Intro]
Yehovah, Mbusa wangadi,
Ndalibe kusowa;
Andigonetsa bwinoli
Mumsipu wokoma.
[Chorus]
Ku madzi ake odikha
Anditsogolera;
Ndi moyo wanga wofoka
Aulimbikitsa.
[Verse]
Anditsogolera m’njira
Zakulungamazo;
Chifukwa changaay’, koma
Cha dzina lakelo.
[Drop]
Ndipyola kodi chikhwawa
Cha mthunzi wa imfa?
Ndalibe mantha ngati ’Nu
Mundiperekeza.
[Bridge]
Chakudya changa chabwino
Mwandikonzera pha!
Pamaso pa adaniwo
Mudyetse mtimanga.
[Instrumental Solo]
(Music takes center stage here, reflecting on the themes of the hymn)
[Outro]
Mwadzoza mutu wanga ndi
Mafuta okoma,
Mwadzaza chikho changadi,
Inde, chisefuka.
Zokoma ndi zakuyanja
Zidzanditsatako;
Ndikhala m’nyumba ya Mulungu
Ku nthawi zonsezo.
Recommended

Love Again_
piano, intense, time, love

Unspoken Love
acoustic soulful melancholic

Roar of the Quiet
agressive hard metal

Helado Caído
Melancholic, sad piano-driven

Hold On to the Light
Ballad, female, glass

Aku Bahagia
dance pop

Nope!
experimental, electronic

Fauzi dan Wafa
pop cheerful
Synthetic Pulse
instrumental,electronic,synthpop,electronic dance music,synth-pop,electro,electropop

Driving Home
synthwave, minor key, 80s, synth, samples

Sell My Soul
pop dance

My life
voice male, jazz rock, indie pop rock, electro

Dziarra - Forever in Flames
electric dance rock post-hardcore metalcore

Dark study
Dark-R&B, dark-piano, male sad voice, melancholy. dark-violin.

Face the Abyss
death metal speedrap darkwave acapella boom bap

Blindog
pop uplifting

Yanındayım
rhythmic pop heartfelt


